Chiphunzitso Cha M'baibulo

Mukufuna ndani?

Mukufuna ndani? Mariya Magadalene adapita kumanda komwe Yesu adayikidwapo Atapachikidwa. Atazindikira kuti mtembo wake palibe, adathamanga kukauza ophunzira ena. Atabwera [...]